Pinned Tweet
I have personally witnessed this guy build a fridge from scratch. If your fridge has any problems and you need repairs contact him through 0992809108 or 0884944754.
Help rt!
CHXKWXPX retweeted
Messi ndi player wopanda khalidwe, nanga ndi chani wapanga dzulo zija?
ati GOAT, ah my foot.
CHXKWXPX retweeted
Nakotu kamkazi ka " Tap the banner to learn more" kamationjeza mene kayambira since morning mpaka pano eh kaona ngati tilipira😂
CHXKWXPX retweeted
Mulanje, thyolo, phalombe maboma awawa kumbali Yama maid ndiye amayesesa,
Ntchito yamnyumba azimayi ambiri ntownmu amachokera kumeneko
CHXKWXPX retweeted
Ngati tingakwanitse mu 2027 mu let’s start a side business. Your salary will not sustain you in the long run.
CHXKWXPX retweeted
There is a chat about the best Rapper both Venercular and English on the TL, can’t seem to see uyu watulutsa album yakeyu on the list😂😂olo m’modzi omuikapo but the same niggas that defended him kuti ndi dholo💀
CHXKWXPX retweeted
Ubwino wa Twitter ndioti we don't go around looking for news. Nkhani zimatipeza tili phee 😌
CHXKWXPX retweeted
Dating wise . The stage I have reached. I think I am just waiting for Jesus to come back 😂😂😂
CHXKWXPX retweeted
Ataona kuti dzitenga nthawi kuti tichoke pakhomo lamakolo,kuchipinda kwathu angoyamba kusungilako nkhuku zamadzira.
CHXKWXPX retweeted
Some of you are only humble because life hasn't given you a reason to be arrogant yet.






























